30/06/2026
BREAKING NEWS πππππ
Pomwe Amalawi ochuluka ali kusautsika ndikapezedwe Ka ndalama, nawo akulu akulu a sukulu zaukachenjede akwenza fees kuchoka pa 650,000 kufika pa 1.3 million, yomwe ili 100% increase. Izi zakhumudwitsa ophunzirawa ndi makolo chifukwa iwo akuopa kuti akangosidwa ndi bungwe lopereka ngongole Kwa ophunzirawa lomwe ndi Loans board, iwo akhala pachiopsezo choyamba asungitsa kaye malo kaamba Koti sangakwanitse kulipira fees yooo chifukwa yakwera mochititsa mantha.
Sukulu zakwezako pakadali Pano ndi LUANAR ndi MZUNI. Ndipo Pali chiyembekezo kuti sukulu zinazo monga UNIMA, MUST, MUBAS zikhalenso zikupanga zomwezi.
Izi zawakumbutsa anthu momwe anali kusangalala ndi Boma lapita lija la MCP pomwe makolo anali kupititsa ana awo mosavuta kaamba ka mitengo yabwino Ku nkhani ya fees.
MCP BACK 2030 π₯π₯π₯π₯π₯
THE MIGHTY UNIMA MCP WING NEWS π₯π₯π₯