YOUTH Alliance Zomba Ntonya

YOUTH Alliance Zomba Ntonya The Power of Young People to Change the World

10/08/2026

Zomba Ntonya constituency
I Love my constituency lets build it with Love and peace ✌️ ONE LOVE
Big up to My brothers, Poya
Myson Jambo. Not forgetting my sister Abiti Ntonya Mary Banda
ULUMBA NTONYA ZOMBA NEWS
Zomba Ntonya Constituency

Achinyamata ambiri ndi odabwa Poona 1,000,000,000 yonse ikufuna kupita ku police unit yokha.  Iwo akufusa adindo kuti al...
27/07/2026

Achinyamata ambiri ndi odabwa Poona 1,000,000,000 yonse ikufuna kupita ku police unit yokha. Iwo akufusa adindo kuti alongosole kagawidwe ka 1 billion imeneyi chifukwa zikuoneka kuti ndalamayi yachuluka unless ngat akufuna kumanga police station not police unit.

Kumbali ya phungu wa Dera la Zomba ntonya sanayankhulepo kathu za kuchuluka kwa ndalamayi ngakhale achinyamata ambiri akudandaula pa Whatsapp group pomweso iyeyo alipo limodzi ndi ma counselor ake. chete ameneyo akukaitsa chinachake

Address

Zomba

Telephone

+265883665801

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when YOUTH Alliance Zomba Ntonya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to YOUTH Alliance Zomba Ntonya:

Shortcuts

Share