Tiuzeni Maganizo Anu

Tiuzeni Maganizo Anu Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tiuzeni Maganizo Anu, Box 96, Phalombe.

Pulezidenti Peter Mutharika wanena kuti iye ali kumbuyo kwa Komiti yoona zosankha anthu maudindo a boma ku parliament(PA...
14/03/2026

Pulezidenti Peter Mutharika wanena kuti iye ali kumbuyo kwa Komiti yoona zosankha anthu maudindo a boma ku parliament(PAC) yomwe ikufufuza pazakugulitsidwa kwa hotelo ya Amaryllis kupyolera mu ndalama zomwe zimasungidwa ndi bungwe loona za anthu ogwira ntchito m'boma.
Mutharika wati iye akutsatira nkhaniyi mwachidwi ndipo aonesesa kuti chilungamo chitsatidwe.

Komitiyi Khalapampando wake ndi Baba Steve Malondera.
Inuyo mukutipo bwanji? Kodi APM wabwera panthawi yake yomwe amafunika kutero kapena akanadikira kaye aone chitsogolo chake?

TIMVE KWA INU👂👂👂Akuti President Mutharika walamula kuti pakuyenera kuchitikanso kafukufuku wina pa zomwe zinachititsa ku...
24/02/2026

TIMVE KWA INU👂👂👂
Akuti President Mutharika walamula kuti pakuyenera kuchitikanso kafukufuku wina pa zomwe zinachititsa kuti ndege yomwe anakwera yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino igwe ndikupha anthu 9 omwe ndikuphatikizapo Wachiwiri kwa mtsogoleriyu a Saulosi Chilima.

Inu mukuona kuti ndi zofunikadi kutero kapena ayi?

23/02/2026

Dziko la Malawi lakhala pa nambala 8 pokhala dziko lomwe likulamuliridwa bwino muno mu Africa. Dzikoli lakhala pa nambala 71 pa dziko lonse lapansi.
Izi zikuchitika patangopita miyezi yochepa President Peter Mutharika atangotenga kumene mpando wautsogoleri wadziko lino.

Tiuzeni ndemanga yanu pankhaniyi..

18/11/2025

PHALOMBE NORTH EAST SPEECH ON PRESIDENT'S PETER MUTHALIKA SONA TODAY ON 18 NOVEMBER 2025


゚viralシfypシ゚viralシalシ

28/10/2025

THANK YOU PEOPLE OF PHALOMBE NORTH EAST

With Your Votes You Have Shown Trust and Love. Wilfred Mpisa Will Work With Everyone To transform This Constituency

SEALED NOW!!

゚viralシfypシ゚

26/10/2025

Ntchito iyambike pa ground tsopano.

Address

Box 96
Phalombe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tiuzeni Maganizo Anu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share