Mr Citinnati

Mr Citinnati Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mr Citinnati, Box 96, Phalombe.

11/09/2026

๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ LERO Mโ€™MBUYOMU โ€” TODAY IN HISTORY
๐Ÿ“… 11 SEPTEMBER
Zochitika zofunika pa 11 September:

1.๐Ÿ‘‰11 September 2001: Ndege zobedwa zinagunda World Trade Center ku New York ndi Pentagon, ndipo ndege ina inagwera ku Pennsylvania. Anthu pafupifupi 3,000 anamwalira pa ziwopsezozi. ๏ฟฝ
Kiwix Server

2.๐Ÿ‘‰11 September 1973: Gulu lankhondo lotsogozedwa ndi Augusto Pinochet linachotsa boma la Purezidenti Salvador Allende ku Chile. Allende anamwalira patsiku limenelo. ๏ฟฝ
History Guesser

3.๐Ÿ‘‰11 September 1297: Asilikali a ku Scotland motsogozedwa ndi William Wallace ndi Andrew Moray anagonjetsa gulu lankhondo la England pa Battle of Stirling Bridge. ๏ฟฝ
History Guesser

4.๐Ÿ‘‰11 September 1609: Wofufuza malo Henry Hudson anafika pachilumba chomwe masiku ano chimadziwika kuti Manhattan. ๏ฟฝ
Kiwix Server.

NKHATA-BAY COMMUNITY RADIO VS PHALOMBE FM.Liwu lakutwosyekaaa!!
30/06/2026

NKHATA-BAY COMMUNITY RADIO VS PHALOMBE FM.

Liwu lakutwosyekaaa!!

Nthawi imeneyo timati mbatata yamu uvuni.
16/06/2026

Nthawi imeneyo timati mbatata yamu uvuni.

Travel mercies biggie. Ife timadalira inuyo.Arthur Peter Mutharika
12/06/2026

Travel mercies biggie. Ife timadalira inuyo.
Arthur Peter Mutharika

Eish, zitafika apa mungatani?
12/06/2026

Eish, zitafika apa mungatani?

MUKUONA BWANJI?
10/06/2026

MUKUONA BWANJI?

KODI MUKUDZIWA?Tsiku ngati lero 10 June koma m'mbuyomo๐Ÿ”น 1940 โ€“ Dziko la Italy linapita ku nkhondo ya World War II motsog...
10/06/2026

KODI MUKUDZIWA?

Tsiku ngati lero 10 June koma m'mbuyomo

๐Ÿ”น 1940 โ€“ Dziko la Italy linapita ku nkhondo ya World War II motsogozedwa ndi Benito Mussolini, kulowa kumbali ya Germany.
๐Ÿ”น 1967 โ€“ Nkhondo ya Six-Day War inatha, Israel ikupambana nkhondoyi motsutsana ndi mayiko angapo a Arab.
๐Ÿ”น 2003 โ€“ NASA inalengeza kutumiza rover ya Spirit Rover kupita ku Mars kukafufuza za moyo ndi chilengedwe cha kumeneko.

๐Ÿ”น 2024 - Ku Malawi, Saulos Klaus Chilima yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko anamwalira pangozi yandege pamodzi ndi anthu ena 8.

05/06/2026

๐Ÿ“œ LERO Mโ€™MBUYOMO (June 5) ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ
๐ŸŒ 1. Tsiku la Chilengedwe Padziko Lonse
Lero ndi tsiku la World Environment Day.
Linakhazikitsidwa ndi United Nations mu 1972.
Cholinga chake ndi kulimbikitsa kusamalira chilengedwe ๐ŸŒณ.
๐Ÿ›๏ธ 2. 1967 โ€“ Nkhondo ya masiku 6 inayamba.

Six-Day War inayamba pakati pa Israel ndi mayiko ena.
Inatha patatha masiku 6 koma inasintha mbiri ya dera limenelo.

๐Ÿ‡บ๐Ÿ‡ธ 3. 1968 โ€“ Robert F. Kennedy anawomberedwa atangowina chitsankho ku Califonia.

Robert F. Kennedy anawomberedwa ku Los Angeles.
Anamwalira tsiku lotsatira.

๐Ÿฅ 4. 1981 โ€“ HIV/AIDS inayamba kudziwika.

Centers for Disease Control and Prevention inalengeza za matenda a HIV/AIDS koyamba.

๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ 5. 2025 Mtsogoleri wakale wa dziko la Zambia Edgar Lungu anamwalira ndipo kufikira lero thupi lake silidalowe mmanda.

04/06/2026

Mau Odzukira (Morning Devotion) ๐ŸŒ…๐Ÿ™
Lemba la lero:
โ€œMโ€™mawa, Ambuye, mumva mawu anga; mโ€™mawa ndidzabweretsa pemphero langa kwa inu, ndipo ndidzayembekezera.โ€ โ€” (Masalimo 5:3)
๐ŸŒฟ Uthenga wa lero
Mโ€™mawa ndi nthawi yabwino yolumikizana ndi Mulungu. Ndi nthawi yomwe mtima uli chete ndipo titha kumva bwino mawu a Mulungu. Monga momwe Davide amanenera, tiyenera kuyamba tsiku lathu ndi pemphero ndi chiyembekezo.
Mulungu akufuna kuti tiziyamba tsiku lililonse tikumudalira Iye, osati mphamvu zathu zokha. Ngakhale mukukumana ndi mavuto kapena kusowa chiyembekezo, kumbukirani kuti Mulungu ali nanu ndipo adzakutsogolerani.
๐Ÿ™ Pemphero
Ambuye Mulungu, zikomo chifukwa cha moyo ndi tsiku latsopano. Ndikupempha kuti munditsogolere mu zonse zomwe ndichite lero. Ndithandizeni kukhala munthu wokhulupirika, wodzichepetsa, komanso wokonda ena. Ndikudalira Inu, chifukwa Inu ndinu mphamvu yanga. Amen.
๐ŸŒผ Mfundo yoti muganizire
โžก๏ธ Yambani tsiku lanu ndi Mulungu, ndipo tsiku lanu lidzakhala ndi mtendere ndi cholinga.

All the best to All Form 2 Students.
01/06/2026

All the best to All Form 2 Students.

Address

Box 96
Phalombe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr Citinnati posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share