Lisah's"" Library ""

Lisah's"" Library "" The story writter

24/03/2025

CHOYAMBIRA INU PANGAN LIKE/FOLLOW PAGE INO KENAKO PANGAN SHARE THEN YAMBANI KUWERENGA.



Part 1

*Linali Sunday pomwe Angela anali kugona pa ped pake km ali mkati mogona phone yake inalira monyinyilika anadzuka nakagwira phone ija koma k*ti adziyankha phone inadzidula.. the same time Angela anapanga check nthaw kupeza k*ti ili 08:15AM..

*Ohh kod mpaka kwacha chonchi anadzifunsa Angela kwinaku ak*tsika pogona...

*Apa Angela anapita kubafa kukangosukusula kunvala zonvala zabwino kuzikonzekeretsa natenga bible lake kuwuyamba waku church anapita panja k*tenga galimoto lake kuwuyamba ulendo.. mdyomba ndikupita Ku Church aliyense ondifuna muuzen k*t sindili around osalora munthu kulowa kumpanda ok and take care of yourself. Anatero Angela kumuuza get man wake..

*Ok madam ndakunvan chilichonse chikhala bwino Pano osadandaula ndithu.. anayankha get man kwinaku akukatsegula get.

*Mosakhalitsa Angela anaiyambadi ulendo wake km atayenda pang'ono anafika pakachipululu pomwe anaona mnyamata patsogolo pake akuyenda wapasi.. apatu Angela anaganiza zoti ayime amutenge mnyamata uja. Atayandikura pomwe pamayenda mnyamata uja Angela analiza hutalii. Pp pp kenako mnyamata uja anatembenuka ndipo anaona munthu mugalimoto akumuyitana.

*Kod mukundiyitana ineyo??? Anafunsa mnyamata uja modabwa..
*Eya kumne ndikuyankhula ndiiweyo kapena iwe ukuonapo munthu wina apa kupatula iweyo ndiineyo???? Anayankha Angela
*Aaaa ayi kungot ndi mmene mukuonekera ndizopeleka chikaiko Kwa ineyo k*t zoona mwaimira ineyo apapa.. anatero mnyamata uja akupita chifupi ndipomwe panayima galimoto paja.

*Angela anamuyang'anitsita mnyamata mwachidwi ndipo anayamba kumwetulira ekha. Eeee km to say fact this is very handsome anaziyankhulira Angela kwinaku akumangomweturira...

PART IS LOADING.....

Ikunveka bwanj??? Osayiwara k*t panga follow k*t tionere limodz k*ti zinatha bwanj in this

Search 's"" Library

18/03/2023



Part 2

Mlembi Lisah

Lisah's Library
WhatsApp: +27834363004

Mwanthaw zonse inu tangopangan follow komanso like page ino k*t nkhaniyi muyimalidzitse k*tinso izikupeza mwa easy...

Mu part 1 tinalakeza apa..

😭😭😭😭😭 Analira abale mwana mosweka mtima ndimonvetsa chisoni uku asakunvetsetsa k*t zikukhala bwanj mwina akulota...

Ali mkat molira f***y anaona panja galimoto ija itayima atasunzumira anaona muk*tsika bokosi lamtengo wapamwamba kwambiri likuchita kunyezimira pamwamba pa Pali maluwa okongola kwambiri....

Abaletu ine nditaona izi mtima wanga unapitilira kupweteka koopsa poganizira mavuto omwe timakumana nawo nthawi zambiri kumasowa zakudya kumachita kusowa pogona mayi anga kumachita kufunda kachitenje kong'ambika km lero Mai anga amwalira kwabwera chinyumba chodula kwambiri momwe awagonekamo mayi anga mtima wanga unali osweka km pot ndinalibe mphavu ina iliyonse ndinangozisiya mmanja mwa Mulungu...

Ngakhale zinali zinthu zopweteka kwambiri f***y analira km anafika povomereza k*t bas mayi Ake apita ndipo or alire bwanj sangabwererenso anangokhala mwana wamkaz akulira mosisima kwinaku akudikira k*t mwambo uchitike iye ayambe moyo wina bas.

Km ali chikhalire pomwe anakhalapo anaona munthu wina owoneka molemekezeka kwambir ndiwa ndrama atavara bwino akuchita kununkhira perfume wa pamwamba wantengo wapatali akupita pomwe iye anakhalapo. Km f***y ataona munthu akufika panali iyepa anali ndi mafunso k*t kod awa akufuna Chan nankha achokera k*tiko....

Ali mkat molingalira anadabwa atagwidwa ponkono ndi munthu uja... Hello f***y ndikudziwa uli odabwa kuona nkhope yachilendo pamanso km usadabwe siine mlendo Okey.... Ohhh ok ndakunvan nde ndiuzen k*t ndinu ndan ndipo mukufuna Chan??? Anafunsa f***y uku akuwang'anitsitsa bamboo aja mwachidwi...

Chabwino ndizilongosore motere f***y mtima wanga ndiosweka πŸ’”πŸ’”πŸ’” ndipo maso anga azaza ndi ntsinje wamisonzi 😭😭😭 ndizinthu zot zikundivuta kunvetsa ndipo sindikudziwa k*t ndiyiwara bwanj pak*t ndaluza munthu yekhayo yemwe anasala pabanja langa......

F***y anawayang'ana bambo aja kuwakweza kuwatsitsa kuli kupweteka Kwa mtima ndizomwe anayankhuka bambowa potengera mmene lyeyo ndi mayi Ake ankavutikira ndimmene bambowa amaonekera. Kumapeto kwake f***y anafunsa ( nde mwat mwaluza munthu yemwe anasala pabanja panu???)

Apatu bambo aja chisoni chinawagwira pomuona f***y nsinkhu wake komanso fundo zomwe akuyankhula... Eee eya ndichonchodi.. anayankha bambo aja mwakachibwibwi choncho.

Okey sir ndakunvan ndithu m***a kupita ngt Pali zokambirana tikumana after mwambowu pepan ngt ndayankhula kuyipa.. anatero f***y apa misonzi itayambanso kulengezera mmaso mwake poganizira k*t moyo wake uyenda bwanj payekha..

Chabwino ntsikana ndisanachoke ndikuuze k*t ndine Mr Benson achimwene wawo wa malemu mayi ako pepa pachilichonse chomwe ndakhala ndikupanga ndikudziwa k*t umavutika ndi mayi ako pomwe ine ndinkasangalala Ku town ko km chomwe ndikufuna ndikuk*tenga k*t ndizipita nawe Ku town k*t mzimu wa malemu mayi ako udziusa muntendere

F***y atanva izi anawayang'ana Mr Benson mwachidwi ndi mokwiya kwambiri misonzi ik*tsika mmaso mwake ngt ntsinje ndipo anat.

Next part 3 is loading.......

Osawira kupanga follow komanso like page ino k*t nkhaniyi muyimalidzitse k*tinso izikupezan mwa easy mwakoma nonse

17/03/2023



Part 1

Mlembi Lisah

Lisah's"" Library
WhatsApp: +27834363004

Iyi ndinkhani yomwe inali yopweteka kwambiri pa moyo wantsikana wina yemwe anayamba kukumana ndimavuto akulu adakali wachichepere zinali zopweteka ndizonvetsa chisoni km kumapeto kwake misonzi yake inasanduka chimwemwe tiyen tiyitsatire nkhaniyi mwachidwi popanga follow komanso like page ino...

F***y anali tsikana wazaka 9 zakubadwa mk*t apa anali ali std5 f***y amakhala ndi mayi Ake okha pok*t bambo Ake anamwalira iyeyu asanabadwe f***y amakhala moyo ovutika nthawi zambiri amatha kupita Ku school osadya penanso kujomba kwenkwen kamba kazovutika zina km ngakhale zinali chomwechi f***y anali ntsikana wanzeru ndiolimbikira maphunziro..

Ndinali ndili mkalas ndikuphunzira km from no where thupi langa linadzidzidwa kwambiri zinandivuta k*t ndiyankhule kapena kusuntha/kugwedweza thupi zinandichitikira izi Kwa ma minutes angapo kenako ndinakhanzikikano km mtima wanga unali wamantha kwambiri ndizomwe zinandichitikirazi ndinayamba kumaganiza zinthu zambiri zosakhala bwino kufikira pomwe ndinaganiza zobwerera kunyumba..

Apatu zitachitika izi f***y sanachedwe koma kupita Kwa aphunzitsi kukatsanzika k*t sakupexa bwino ndipo aphunzitsi anamulora k*t apite akapume anayenda mwana wamkaz mwachangu kwambiri mtima wake usali mmalo km anali odabwa asanafike kwawo kuona k*t Kuli anthu ambiri kwambiri zomwe zinapereka mafunso mumtima mwake... Kod anthuwa akufuna Chan kunyumbaku???? Anadzifunsa f***y km mwamantha uku akupitilirabe ulendo wakomweko....

Apa nditafika mtima wanga unayamba kubaya kwambiri pozindikira k*t ndikuyenera kunva uthenga osakhala bwino sindinafune kuyankhulana ndi wina aliyese km kuyenda straight mpaka kuchipinda komwe kumakhala mayi anga..

F***y anali odabwa atafika kuchipinda kuja kupeza k*t mayi Ake kulibe ndipo kwazaza azimayi ankhope zachisoni zokhazokha apatu f***y sanapilire mmalo mwake mwana wamkaz anayamba Kulira😭😭😭😭 mosweka mtima poganizira k*t mayi Ake bas kulibe

F***y(mosweka mtima anafunsa) kod wina wake angandiuze k*t chikuchitika ndichan pakhomo pano????

Km zinali zopweteka Kwa f***y kuona anthu onse Ali zii popanda ngakhale munthu mmodz oyankha mk*t apa nawo anthu ataona nkhope ya f***y ndi sinkhu wake anali atadzadzidwa ndichisoni. Kenaka f***y ananva panja panyumba pakubwera galimo km mugalimoto munali mukuyimbidwa nyimbo zachisoni kwambiri apatu mwana wamkaz analiraπŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’” ngt wakwezedwa volume kwinaku akuchita kuzing'ambira zovara zomwe anavara pathupi pake...

Apa mayi mmodz anadzuka pomwe anakhala ndipo anamugwira f***y pakono namuyang'ana mwachisoni Ku nkhope kwake ndipo anati.... Pepa ntsikana limba mtima pak*t kwamulungu ndikomwe ndinachokera ndikomwenso tikuyenera kubwera..😭😭😭Mai ako bas kulibe...

😭😭😭😭😭😭Analira abale mwana mosweka mtima ndimonvetsa chisoni uku asakunvetsetsa k*t zikukhala bwanj mwina akulita..

Mmmm km guy's moyo kusinza nkhaniyi ikupitilira mu part 2 tapangan follow page ino k*t MUTHE kuyitsatira bwino kod nanga ikunveka bwanj??????

ABALE TIGWIRANE MANJA POWAIKIZA MMAPEMPHERO ANZATHU OMWE AKHUNZIDWA NDI MADZ..TALUZA MAKOLO ANA ATHU AZIBALE ATHU KATUND...
16/03/2023

ABALE TIGWIRANE MANJA POWAIKIZA MMAPEMPHERO ANZATHU OMWE AKHUNZIDWA NDI MADZ..

TALUZA MAKOLO ANA ATHU AZIBALE ATHU KATUNDU WATHU NDIZINA NGT IWE ULI MOYO NGT WAPUKUMUKA KU CHILANGOCHI TANGOTENGA 1MINUTE NDIKUMUKWEZA MULUNGU WAKUMWAMBA SIIWE OPAMBA AYI KM MULUNGU WAKUKONDERA..

OSAYIWARA KUPANGA LIKE PAGE INO KOMANSO SHARE K*T ANZATHU ENA ATHENSO K*TITHANDIZA KUWAYIKIZA MMAPEMPHERO ABALE ATHUWA.

Address

MW MH MJ
Mangochi

Telephone

+27834363004

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lisah's"" Library "" posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Lisah's"" Library "":

Share

Category