Copyright Society of Malawi

Copyright Society of Malawi An all-embracing copyright society with over 11,000 individual rightsholders and 11 member associations

23/07/2026
23/07/2026

Akuti nyimbo yakuti ndaladira K1,000 ina K500 afunseni total amount yomwe alandira akuuzeni..

Tiyeni anthu tiwauze zoona!

23/07/2026

Trending and royalties distribution ndizosiyana. Tikapeza nthawi Call or WhatsApp kuti tizimvetsetse zinthuzi..
4368 / 0 987 045 429

23/07/2026

COSOMA si YouTube! COSOMA si Spotify!

Zinthuzi ndizosiyana. Ma Royalties sakhudzanako ndi zimenezi.

23/07/2026

Zama Royalties zimangofunika kumvetsetsa kuti zimakhala bwanji.

Call or WhatsApp
4368 / 0 987 045 429

22/07/2026

ZA KAGAWIDWE KA MA ROYOTE

Ngati pali chinthu chomwe tikuyenela kumvetsa ndichakuti, COSOMA ndiyomwe imaulutsa maina a ma membala omwe apezeka pa top 10 ndipo ma royote akamagawidwa timagawa momwe zinthu zilili.

Tiyeni timvetse kuti gender ndi kagawidwe ka ndalama’zi ndi zinthu ziwiri zosiyana, komanso kagawidwe ka ma royote’wa tilibe malamulo owonetsa kuti poti awa ndi azibambo alandire motere, kapena kuti ndi amayi alandire motere, kapena kuti pa top ten pakhale azimai motere, ndipo azibambo apezekepo motere.

Ife a bungwe la COSOMA timagawa ma royote’wa momwe zinthu zikuyenela kukhalira, choncho tiyeni tisamachione chinthuchi molakwika kuti mwina zinakatere, chachikulu tiyeni tidzilimbikira kuti tichiteso bwino.



22/07/2026

KODI BLANK MEDIA LEVY NDI CHANI??

Blank Media Levy ndi ndalama zomwe eni ufulu wa ntchito za luso amalandira ngati chipepeso (kapena kuti compensation) kuchokera ku ndalama zomwe zimasonkhanitsidwa pa zinthu zosungiramo ntchito za luso ngati ma CD, flash disk, memory card, ma computer ndi zina, chifukwa ntchito zawo zimatha kukopedwa kapena kusungidwa pa zinthu zimenezo kuti zigwiritsidwe ntchito paokha.

Pali funso ngati?
Funsani kuti mumvetsetse.

A MUST READ!!!
22/07/2026

A MUST READ!!!

NDONDOMEKO YOGAWA MA ROYOTE A BLANK MEDIA LEVY OYAMBIRA APRIL, 2025 MPAKA MARCH, 2026.
20/07/2026

NDONDOMEKO YOGAWA MA ROYOTE A BLANK MEDIA LEVY OYAMBIRA APRIL, 2025 MPAKA MARCH, 2026.

PRESENTATION OF BLANK MEDIA LEVY ROYALTIESToday, the Copyright Society of Malawi (COSOMA) proudly celebrates another mil...
20/07/2026

PRESENTATION OF BLANK MEDIA LEVY ROYALTIES

Today, the Copyright Society of Malawi (COSOMA) proudly celebrates another milestone in empowering Malawi's creative industry through the presentation of the 2025/2026 (April 2025 - March 2026) Blank Media Levy Royalties.

Blank Media Levy is a form of compensation provided to creators for the private copying of their copyrighted works. The levy is collected by the Society in collaboration with the Malawi Revenue Authority (MRA). This is done from the importation of storage devices capable of copying music, films, books and other protected works.

This year's disbursement of over MK1.8 billion demonstrates our unwavering commitment to protecting intellectual property rights, rewarding creativity, and contributing to the growth of Malawi's creative economy in line with the aspirations of Malawi 2063.

Congratulations to the top earners and all beneficiaries.

Creativity Rewarded. Rights Protected. Malawi Inspired.



Address

Lilongwe
POSTOFFICEBOX30784

Opening Hours

Monday 07:30 - 16:30
Tuesday 07:30 - 16:30
Wednesday 07:30 - 16:30
Thursday 07:30 - 16:30
Friday 07:30 - 16:30

Telephone

+2651751148

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Copyright Society of Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Copyright Society of Malawi:

Shortcuts

Share