Malawi wanga

Malawi wanga This is the Entertainment Arm of .Trending updates on malawian celebrities,Entertainment,News and many more
✔️ Follow
✔️Like
✔️Share
(4)

Hie malawi wanga Ndine Jane wazaka 24 from zingwangwa . ndikufuna mamuna wa  serious ok*ti azinditenthetsa  munyengo yoz...
18/09/2026

Hie malawi wanga
Ndine Jane wazaka 24 from zingwangwa . ndikufuna mamuna wa serious ok*ti azinditenthetsa munyengo yozizilayi. Should be around Blantyre or ma boma ozungulira, akhale wa zaka za pakati pa 30 to 36, at least oti ku school anafikako, yes ozindikilako ndithu like yemwe anapondako ku college komaso akhale ndi galimoto k*t tidzitha kuvaya out Ine ndimakhala ndi auntie koma am ready k*tulukamo nyumba yawoyi. Mamunayo akhale ready for hiv test.

18/09/2026

Ngati umakhulupira k*ti Mulungu adzasintha nyengo zako zonse
Tangolemba AMEN

Ndikugawa uthengau kuma group atatu

mwamva kumeneko
18/09/2026

mwamva kumeneko

18/09/2026

Good morning 🌄
Jumah Mubarak

 Police ya Thyolo yamanga a Chisomo Andrew, adzaka  27,  atapezeka akugwililira mwana wadzaka 4 kumandaNkuluyu anthu ana...
18/09/2026


Police ya Thyolo yamanga a Chisomo Andrew, adzaka 27, atapezeka akugwililira mwana wadzaka 4 kumanda

Nkuluyu anthu anamupeza pa 15th September, 2026 Akuchita kusaweluzikaku ndi Azibambo ena Amene adamva kulira kwa mmwana mmandamo ndipo atathamangila anamupeza nkuluyo Ali jijiri jijiri ndikamwanako


.....chonena tilibe nafe zoopsa izi 😭😭

18/09/2026

from inbox
Hello malawi wanga Chonde ndiyikeni nchigoba tandifunsireko mankhwala ochotsa mimba chonde mwamuna wandikana 😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔

kwacha😂
18/09/2026

kwacha😂

17/09/2026

Naye satana pano wadura kuphudzira ufiti mpaka 700k 😂

  Mustafa Shaibu yemwe amadziwika ndi dzina loti Mofolo popanga ma comedy ndi Anganga Afick wamwalira pangozi yomwe yach...
17/09/2026


Mustafa Shaibu yemwe amadziwika ndi dzina loti Mofolo popanga ma comedy ndi Anganga Afick wamwalira pangozi yomwe yachitika pa Mbulumbuzi
mzimu wawo uwuse muntendere

Wapezeka lero ndipo ali moyoNzika ya ku Britain, Nasrat Osman uja yemwe apolice akhala ak*tumiza ma uthenga k*ti Amene a...
17/09/2026

Wapezeka lero ndipo ali moyo

Nzika ya ku Britain, Nasrat Osman uja yemwe apolice akhala ak*tumiza ma uthenga k*ti Amene angamuone kapena kudziwa anthu omwe anamusunga alandila chionamaso cha 30 million uja wapezeka mayiyu anabedwa ku Mount Pleasant Lachisanu lapitali, wapezeka ali bwino pakalipano wabwerera kwawo amene wasimikiza izi ndi mchimwene wake Shobi Jiwa

Congratulations Malawi Police ntchito mwaigwira ngakhale a Deputy Inspector General Noel Kaira anaombeledwa pogwira ntchitoyi koma akwanitsa kumpulumusa Nasrat Osman

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi wanga posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Malawi wanga:

Shortcuts

Share