Democratic Progressive Party - DPP

Democratic Progressive Party - DPP This is the Official page of the Democratic Progressive Party in Malawi The Democratic Progressive Party (DPP) is a political party in.
(5)

The party was formed in February 2005 by Former President of the Republic of Malawi, His Excellency Ngwazi Professor Bingu Wa Mutharika.

04/06/2026

Zina Ukamva
On Bob Chimkango's car shooting before election

Yao Version:*Chidziwitso cha DPP Diaspora Wing RSA - 03 June 2026**Mautenga ga Magalimoto ga Kubwelera Kwawo*1. *Chenjez...
03/06/2026

Yao Version:

*Chidziwitso cha DPP Diaspora Wing RSA - 03 June 2026*
*Mautenga ga Magalimoto ga Kubwelera Kwawo*

1. *Chenjezo la achinyengo*: Boma likanapangabe mundu kapena bungwe lililose kupeleka magalimoto ga kubwelera kwawo. Pali antu akusambalila utenga wa udesi kuti magalimoto galipo soni akuwombela ndalama. *Mungapeleka ndalama kwa mundu jwalijose*.

2. *Umu lisasamalile*: Pakuŵa magalimoto ga kubwelera, boma ni liŵawalanjile WaMalawi wosope kupitila m’malango ga mwakuwona soni liŵa na ndondomeko syakusosekwa.

3. *DPP Diaspora*: Tuli na akulondolola m’malo gosweleka kuti atapate antu. Mkonanaje nao pa manambala gawe.

4. *Manambala ga kupelekela idini:*
- *Balozi ya Malawi, Pretoria*: 012 342 0146
- *Consular General, Johannesburg*: 011 234 8577
- *DPP Diaspora RSA Wing*: Governor 083 478 8711, Recruitment Director 083 516 9730, Publicity Secretary 067 167 8824
- *Akulondolola DPP*: King Kush Cape Town 074 204 2533, Khansala I.W. Malekano George/Cape Town 064 165 7736, Kochoka Durban 081 472 4268

*Malipili*: Atamanyisiye Akefe Sukali Mviza, Publicity Secretary.

Mwachidule: Mundu jwalijose akuwombela ndalama “magalimoto ga kubwelera” lelo ni achinyengo. Mujilinjilile utenga wa boma.

Unungaga kuyanika ndisimulile mu audio ya Chiyao soni?

Uthengawu tifikitsireni kujoniko
03/06/2026

Uthengawu tifikitsireni kujoniko

03/06/2026

MCP ndi Chakwera anayesetsa kungoti DPP ndi system

The Minister of Finance ,Economic Planning and Decentralisation Hon Joseph Mathyola Mwanamvekha has just arrived at BICC...
03/06/2026

The Minister of Finance ,Economic Planning and Decentralisation Hon Joseph Mathyola Mwanamvekha has just arrived at BICC for the much anticipated National Economic Recovery Plan Consultative Meeting .

Some notable faces from the government side include The Chief Secretary , Dr Justin Adakki Saidi, The Minister of Information , Dr Shadreck Namalomba , The Governor of the Reserve Bank Dr George Partridge .

The President of Bankers Association of Malawi, Mr Philip Madinga is the facilitator of the workshop.

National Consultative Workshop on the National Economic Recovery Plan (NERP) 2025–2030 – Tomorrow at BICC, LilongweThe H...
02/06/2026

National Consultative Workshop on the National Economic Recovery Plan (NERP) 2025–2030 – Tomorrow at BICC, Lilongwe

The Hon. Joseph Mathyola Mwanamvekha, MP, Minister of Finance, Economic Planning and Decentralization, will host a National Consultative Workshop on the Draft National Economic Recovery Plan (NERP) 2025–2030 tomorrow at the Bingu International Convention Centre (BICC) in Lilongwe.

Mr. Phillip Madinga, CEO of Standard Bank Malawi and President of the Bankers Association of Malawi, will co-host and moderate the session.

The workshop brings together government, development partners, the private sector, academia, civil society, and other key stakeholders as Malawi shapes an inclusive economic recovery roadmap under the leadership of His Excellency President Prof. Arthur Peter Mutharika.

All roads lead to BICC.
Come one, come all – it’s happening tomorrow!

 Unduna wa zachuma ndi mapulani a chuma wakonza nkumano, omwe uchitike lachitatu pa 3 June, 2026 ku BICC mu nzinda wa Li...
02/06/2026



Unduna wa zachuma ndi mapulani a chuma wakonza nkumano, omwe uchitike lachitatu pa 3 June, 2026 ku BICC mu nzinda wa Lilongwe, kuti nthumwi zikakambirana za ndondomeko yokonzanso chuma cha dziko lino, National Economic Recovery Plan (NERP) muchingerezi.

Malingana ndi kalata imene undunawu yatulutsa, nkumanowu ndi njira imodzi yofuna kuonetsetsa kuti a Malawi akupatsidwa mpata opereka maganizo awo pa m'mene chuma cha dziko lino chingakonzedwere.

Ku nkumanowu umene wapampando wake ndi nduna ya zachuma ndi mapulani a chuma, Joseph Mwanamvekha, kukakhalanso adindo osiyana-siyana, kuphatikizipo a mabungwe omwe si aboma komanso ma kampani, mabungwe amene amathandiza dziko lino pachitukuko, sukulu za ukachenjede ndi mabungwe akafu-kufuku komanso ochita malonda.

Nduna yowona kuti pakusasiyana pakati pa abambo ndi amayi, wolemekezeka a Mary Navicha alimbikitsa mabungwe omwe si abom...
02/06/2026

Nduna yowona kuti pakusasiyana pakati pa abambo ndi amayi, wolemekezeka a Mary Navicha alimbikitsa mabungwe omwe si aboma kuti azilimbikira kusonkhanitsa chuma ndi thandizo m’dziko muno m'malo modalira kwambiri ndalama za othandizira akunja, kuti ntchito zawo zizikhala zokhazikika komanso zopindulitsa.

Iwo anena izi mu mzinda wa Lilongwe pamene amatsegulira msonkhano wachiwiri wa Umunthu Social Impact Forum komanso kukhazikitsidwa kwa Social Impact Index.

Wolemekezeka a Navicha ati kuchepa kwa thandizo lochokera kunja kwakhudza ntchito za mabungwe ambiri, ndipo msonkhanowu ndi mwayi wabwino wopangira njira zothetsera mavuto amene akukumana nawo.

Mkulu wa bungwe la Thrive Afrika, Wilson Chivhanga, wati m'kofunika kulimbikitsa mgwirizano pakati pa boma, mabungwe omwe si aboma ndi ochita malonda kuti dziko la Malawi litukuke m’mbali zosiyanasiyana.

Nduna yazofalitsa nkhani Dr Shadric Namalomba lero ikuyendera Hotelo yatsopano ya Ryalls yomwe a Nico Group akumanga mun...
02/06/2026

Nduna yazofalitsa nkhani Dr Shadric Namalomba lero ikuyendera Hotelo yatsopano ya Ryalls yomwe a Nico Group akumanga munzinda wa Lilongwe yomwe ikuyembekezeka kupititsa patsgolo chuma cha dziko lino kudzera muntchito zokopa alendo.

Ntchito yomanga hotelo yi yomwe igwiritse ntchito ndalama zokwana USD 60 million ndipo ikhale ndi zipinda zogonamo 180 ikuyembekezeka kufika kumapeto mmwezi wa October chaka chino.

Monga mneneri waboma Dr Namalomba ayendera ntchitoyi ndicholinga choti akhale ndi uthenga olondola wa zitukuko zikuluzikulu zomwe zikuchitika mdziko lino.

NATIONAL CONSULTATIVE WORKSHOP ON THE NATIONAL ECONOMIC RECOVERY PLAN (NERP) 2025–2030The Ministry of Finance, Economic ...
01/06/2026

NATIONAL CONSULTATIVE WORKSHOP ON THE NATIONAL ECONOMIC RECOVERY PLAN (NERP) 2025–2030

The Ministry of Finance, Economic Planning and Decentralization (MoFEPD) wishes to inform the general public and all key stakeholders that the Government of Malawi will convene a National Consultative Workshop on the Draft National Economic Recovery Plan (NERP) 2025–2030 on Wednesday 3rd June 2026 from 8:30 AM at the Bingu International Convention Centre (BICC) in Lilongwe. The Workshop will be chaired by Honourable Joseph Mathyola Mwanamvekha, Minister of Finance, Economic Planning and Decentralisation and will be moderated by Mr. Phillip Madinga, Chief Executive Officer (CEO) of Standard Bank Malawi, President of Bankers Association of Malawi and Board Member of National Planning Commission (NPC).

The National Economic Recovery Plan (NERP) has been developed as a strategic framework aimed at restoring macroeconomic stability, accelerating economic growth, addressing fiscal and debt challenges, enhancing food security, strengthening the external sector, and safeguarding vulnerable populations. The Plan outlines immediate, short-term, and medium-term policy interventions intended to restore economic resilience and prosperity in line with Malawi 2063 aspirations.

The consultative workshop forms part of Government’s commitment to ensuring that the recovery plan benefits from broad-based stakeholder engagement and national ownership. The meeting will, therefore, bring together representatives from:
- Government Ministries, Departments and Agencies (MDAs);
- Development Partners;
- the private sector (MCCI);
- academia and research institutions;
- civil society organizations;
- professional bodies;
- and other key stakeholders.

The Ministry, therefore, wishes to invite the above mentioned stakeholders including the general public to the Consultative Workshop to contribute towards shaping a credible and inclusive economic recovery roadmap for Malawi.

For any further enquiries, please contact Mr. Adwell Zembele, Director of Economic Planning at [email protected] or through phone at +265888145033/+265999145033.

Issued by:
Ministry of Finance, Economic Planning and Decentralization
Capital Hill
Lilongwe

Address

New Naperi
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Democratic Progressive Party - DPP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share