Department of Climate Change and Meteorological Services

Department of Climate Change and Meteorological Services The Official page of the Department of Climate Change & Meteorological Services .

Updates on Weather, Climate, Alerts & News for informed decisions https://bit.ly/m/dccms

🌥️🌥️🌥️ M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 10 OCTOBER 2026Tiyembekezere nyengo yofunda komanso ya mitambo yapat...
09/10/2026

🌥️🌥️🌥️ M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 10 OCTOBER 2026

Tiyembekezere nyengo yofunda komanso ya mitambo yapatalipatali m’madera ambiri usiku uno ndi mawa m’mawa.

Mawa masana, kudzakhala kotentha komanso kwa mitambo yapatalipatali m’madera ambiri koma m’madera ambiri akumpoto kudzakhala kwa mphepo.

Mphepo ikuyembekezereka kuomba mwamphamvu nthawi zina pa nyanja zathu.

MPHEPO: Idziomba kuchokera kumwera chakumvuma.
LAMULUNGU: Nyengo yotentha komanso yamitambo yapatalipatali…

Mukafuna kudziwa nyengo ya dera lanu pangani dowunilodi apu ya zanyengo (zanyengo app) pa foni yanu ya m'manja yomwe mungaipeze pa gugo puleyi sitoro (google play store) pogwiritsa ntchito link iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.zanyengo&pli=1

09/10/2026

Morning Weather with Alex: Find out how your day is looking! Are you ready?

08/10/2026

Evening Weather with Alex: Stay prepared with tomorrow's forecast! How is the weather looking in your area?

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 9 OCTOBER 2026 Tiyembekezere nyengo ya mphepo, yofunda pang’ono komanso mit...
08/10/2026

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 9 OCTOBER 2026
Tiyembekezere nyengo ya mphepo, yofunda pang’ono komanso mitambo yapatalipatali m’madera ambiri usiku uno ndi mawa m’mawa.

Mawa masana, kudzakhala kotentha komanso kwa mitambo yapatalipatali m’madera ambiri koma m’madera ochepa akumwera tiyembekezere mvula yamabingu.

MPHEPO: Idziomba kuchokera kumvuma.
LACHISANU: Nyengo yotentha komanso yamitambo yapatalipatali…

Mukafuna kudziwa nyengo ya dera lanu pangani dowunilodi apu ya zanyengo (zanyengo app) pa foni yanu ya m'manja yomwe mungaipeze pa gugo puleyi sitoro (google play store) pogwiritsa ntchito link iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.zanyengo&pli=1

Admin wa weekend safuna zoyambana ndi agulu. Mukazungulira zongulira ntaunimu mukayendayenda, mukagwira ntchito kapena m...
08/10/2026

Admin wa weekend safuna zoyambana ndi agulu. Mukazungulira zongulira ntaunimu mukayendayenda, mukagwira ntchito kapena mukagulitsa ma bizimesi. Muyime payima anzanu ndikumamwa madzi ochuluka. Kaya ma 5 litres, 2 litres,500 ml, ma 2 handede, 1 handede ndi manchocho handede.

Kumamwa madzitu kumeneko. Koma El Nino iweyo!

Pewani kukhala padzuwa nthawi yayitali.
Komanso anawo azisewera mnyumba kapena panthuzi.

08/10/2026

Morning Weather 08/10/2026

07.10.2026 | 14:00 PMMasana a lero kunatentha kwambiri.Agulu kwa Ngabu ku Chikwawa ulemu wanu☀️
07/10/2026

07.10.2026 | 14:00 PM

Masana a lero kunatentha kwambiri.

Agulu kwa Ngabu ku Chikwawa ulemu wanu☀️

07/10/2026

Evening Weather with Alex

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 8 OCTOBER 2026 Tiyembekezere nyengo ya mphepo, yofunda pang’ono komanso mit...
07/10/2026

M’MENE NYENGO IKHALIRE USIKU UNO NDI MAWA PA 8 OCTOBER 2026
Tiyembekezere nyengo ya mphepo, yofunda pang’ono komanso mitambo yapatalipatali m’madera ambiri usiku uno ndi mawa m’mawa.

Mawa masana, kudzakhala kotentha komanso kwa mitambo yapatalipatali m’madera ambiri koma m’madera ochepa akumwera tiyembekezere mvula yowaza.

MPHEPO: Idziomba kuchokera kumvuma.
LACHISANU: Nyengo yotentha komanso yamitambo yapatalipatali…

Mukafuna kudziwa nyengo ya dera lanu pangani dowunilodi apu ya zanyengo (zanyengo app) pa foni yanu ya m'manja yomwe mungaipeze pa gugo puleyi sitoro (google play store) pogwiritsa ntchito link iyi https://play.google.com/store/apps/details?id=com.zanyengo&pli=1

Air Quality Forecast for Malawi. Valid 7 October to 13 October 2026.
07/10/2026

Air Quality Forecast for Malawi.
Valid 7 October to 13 October 2026.

Address

Victoria Avenue
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Department of Climate Change and Meteorological Services posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Department of Climate Change and Meteorological Services:

Shortcuts

Share