Nkhani ZA KWA Safalao

Nkhani ZA KWA Safalao Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nkhani ZA KWA Safalao, Public & Government Service, Blantyre.

22/04/2020

Ma guys inunso ngat muli nazo nkhani kuma ponya

12/06/2019

Kwa amene timamumu dziwa Andrew mwale watisiya dzulo usiku atagwidwa ndi shock

19/01/2019

Gyz nkhani yachison yango tipeza kumene nyamata amene atchuka kt NYANI koma dzina lake la nchik*ta ndi wiladi wa tisiya.

07/10/2017

Gooooooooo 4-0 kkkkkkkk neba apsye mtima BB WOYEEEEEEEEEEEEH

08/05/2017

kod gyz ndizoona k*t munthu ukafuna kukumba chimbuzi uzikadzisa amfumu?

09/04/2016

Tsikana wina wa kwasafalao dzina lake zeffa watisia dzana.may her soul rest in peace

05/04/2016

Atsikana ena odziwika bwino aphophola m'mawa wa lero pa nsika wa safalao chifukwa chot ana bwekana zuvala nde wina pokumbusa mbasha zake panali kusanvana ayambapo kuithana khonya.Mau awiri kwa atsikana amenewa.

Address

Blantyre

Telephone

0882742762

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani ZA KWA Safalao posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share