Nkhani Zakuchipinda and Other Sex Stories

Nkhani Zakuchipinda and Other Sex Stories Only s*x stories.Lets be open to talk about s*x issues and other stories be free to send us anything wil post it for you.

27/09/2014

amuna anga anasiyila kundigona..kupeza kapambali nndikukakwa?

09/08/2014

dzulo andigona amuna 4 koma ndinaledzela zedi..but am HIV positive..help me how can i disclose my status to these gentlemen? Help me please.ine Maggy from kachele in Blantyre..

01/07/2014

dnt hide my name, am johnson.akazi anga akundikani katundu since match pamenepa kupeza kapambali ndikulakwa?

21/05/2014

faith am 24 years old..Amuna anga ak*t ndizipita kumudzi chifukwa alephela u a MP...ine kumudzi sindingakakhaleko.ndinazowela moyo wa ntauni.chonde amene angasangalasidwe nane undioze.

09/04/2014

amuna anga sakufuna k*t tizigonana monga kale pano mpaka miyezi iwiri.. Ndayesesa kuwadandaulila koma zinthu sizikusintha.. Nane ndi muthu zimandivuta pena..kapena ndingopeza kapambali ndilakwitsa? Ndine janehery kuno ku kwa ka chele ku bulantaya

20/03/2014

ndine Alice and am 23 years old.kuno ku blantyre.last friday ndinapita ku outing ndi ma frinds anga atatu...nkhani ndadza nayo apa ndyot mamuna amene nananditenga k*t tikagonane amfuna ndizimuyamwa chokozela chake and i did as hz wish... Koma koma chandibwesa ine mmawa k*tacha ndapezeka k*t kumaliseche kwangaku kukupwetka kwambri koma ndikulephela kukodza bwinobwin...chonde n ndithandizeni... Pali amene akuziwako mankwala achikuda?

27/02/2014

ndine jane ku mulanje..amuna anga ndayamba kuwadabwa masiku ano sitimagonana monga kale.pano akabwela ku nchito akumakhalila pa screen.kena kugona basi..izi zakhala zikuchitka kwa miyezi itatu pano. Nanu ndi nkazi ma feeling amandipeza.kapena ndipeze nane woti azindithandiza? Pliz help me?

22/02/2014

dnt hide my name ndine martha kuno kwakachere ku blantyer,anthu ine ndithandizeni ine chibwenz changa chinandipatsila matenda pa valentine paja,ndikungotulutsa ukazi kumaliseche kwangaku kumufunsa iye akukana k*t tipite ku chipatala tikayezetse vuto lina ndiloti mamuna wanga akubwela nxt week from south africa, koma akabwela mwina azafuna kunyengana naye.nditani ine kumaliseche kwangaku kukuwawa kwambiri.ndithandzeni ndine mmalawi zanu mapeto ake banja langa litha

10/01/2014

Wawa adm,ndine stela kuno ku mulanje, ndakwatiwa miyezi itatu yapitayi, koma amuna anga akungofuna azindigona tsiku ndi tsiku ine abale ine zanditopetsa komanso ali ndi chida chachikulu ndithu ndikuganiza zoti ndikawaoze ankhoswe athu kapena ndingonamizila k*t ndikudwala? Ndithandizeni abale anga!

11/12/2013

Help this friend out! Kodi ndizoona k*ti kuchindana mukusamba like mutsinje or Nyanja mkazi sangatenge mimba?

07/12/2013

Admin plz, dnt show people my I'd, ndangofika kumene kuchokela ku south africa and mwamuna wanga anthu andioza k*ti wapeleka mimbo kwa mkazi wina wake wosasambanso ngati amenewo, and I dnt knw wt to do now, help me plz I hv money and evrythn that can me to have my own house!

21/09/2013

Chonde wa adm bisani zina langa! Akazi anga anapita ku joweni zaka zitatu zapitazo koma mpaka pano sakubwela, kapena nane ndingopeza ka mkazi kapambali koti kazindithandizaa? Ndikayimba phone amadula amangoti andyimbila koma samayimbaso!

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani Zakuchipinda and Other Sex Stories posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share