A Inno Busy

A Inno Busy 🌍 A INNO BUSY | Afro Artist
🎢 Afrobeat β€’ Afro Fusion
πŸ”₯ Pure Vibes β€’ Real Energy iam music n Iam Reggae Dancehall __
(10)

05/10/2026

Saint-Realest πŸ”₯ πŸ™Œ Eeh

THANK YOU πŸ™ Ndikufuna kuthokoza nonse amene mumakonda nyimbo zanga.Simukundikonda chifukwa ndakugulirani, koma mumandiko...
04/10/2026

THANK YOU πŸ™

Ndikufuna kuthokoza nonse amene mumakonda nyimbo zanga.

Simukundikonda chifukwa ndakugulirani, koma mumandikonda chifukwa nyimbo yanga yakhudza mitima yanu. Izi nde chikondi chenicheni. Izi nde dalitso.

Kwa ine, nyimbo ndi uthenga, ndi dalitso lochokera kwa Mulungu. Ndi talent yachibadwa, siinagule. Chifukwa chake sindifunika kukugurani kuti mundikonde. Ngati mumandimvera, mumandigawana, mumandipempherera - ndinu banja langa.

Zikomo pondikhulupirira. Zikomo pondikonda. Nyimbo zambiri zabwino zikubwera chifukwa cha inu.

Ndimakukondani kwambiri! πŸ™πŸΎπŸŽΆ
A inno Busy

03/10/2026

Watch My New Video πŸ“₯ (Link in comment box)

🚨 KE NOW OUT, 🚨
02/10/2026

🚨 KE NOW OUT, 🚨

Malawian Raw Talent __ KE is the song concerning about Love BirdsC...

30/09/2026

4 koloko koma chidzuwa chonchi? πŸ™„ Leronso kwanyanya!

30/09/2026

Mwadzuka bwanj? What's good Today!!

28/09/2026

🚨 KE official Music Video 🚨

🎬 SAVE_THE_DATE
02_10_26

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A Inno Busy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to A Inno Busy:

Shortcuts

Share