08/06/2026
๐ฟ๐ฒ CHADIZA EAST UPDATE FOR Hon. Olivia Phiri-Chadiza East constituency
Tikupitiliza kufikira anthu m'madera osiyanasiyana a Chadiza East, kumvera maganizo awo ndi kukambirana njira za chitukuko. Zikomo kwambiri chifukwa cha chikondi, support ndi kulandira bwino komwe mukutipatsa.
Pamodzi titha kupanga Chadiza East kukhala malo abwino kwa aliyense. Tiyeni tipitirize kugwira ntchito limodzi chifukwa maendeleo amachokera ku mgwirizano.
"Voice ya anthu, ntchito ya anthu, chitukuko cha anthu." ๐ช๐พ๐ฟ๐ฒ