Emmanuel Chisawa

Emmanuel Chisawa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Emmanuel Chisawa, Eastern Cape, Blantyre.

Ukakhala ovuta ndi choncho, ukagwa mmavuto palibe amakuthandiza coz kungoti wavuukamo mmenemo ndi ngozi kwa othandizawo😁...
02/10/2026

Ukakhala ovuta ndi choncho, ukagwa mmavuto palibe amakuthandiza coz kungoti wavuukamo mmenemo ndi ngozi kwa othandizawo😁

Kumakhala bwino ndiwanthu

Vladimir Putin wanena kuti dziko la Iran ladzidzimutsa dziko lonse lapansi."Dziko lonse lapansi ladabwa ndi kulimba mtim...
02/10/2026

Vladimir Putin wanena kuti dziko la Iran ladzidzimutsa dziko lonse lapansi.

"Dziko lonse lapansi ladabwa ndi kulimba mtima, komanso kupilira kwa anthu a ku Iran."

Ndipa 10 October tu mpweteko will be backšŸ”„šŸ”„
02/10/2026

Ndipa 10 October tu mpweteko will be backšŸ”„šŸ”„

WAPOLISI WADZIPHA M'BOMA LA NTCHEU Wapolisi wophunzitsa pa sukulu yophunzitsira apolisi ya Mtakataka ku Mlangeni m'boma ...
02/10/2026

WAPOLISI WADZIPHA M'BOMA LA NTCHEU
Wapolisi wophunzitsa pa sukulu yophunzitsira apolisi ya Mtakataka ku Mlangeni m'boma la Ntcheu, Gilbert Mwalwanda, wazaka 31, wadzipha pa zifukwa zomwe sizikudziwika.

Mneneri wa Polisi ku Ntcheu, Inspector Jacob Khembo, watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati apolisi adalandira lipoti la imfa ya mnzawoyo m'mawa wa lero.

Khembo wati kafukufuku woyambirira wasonyeza kuti Mwalwanda adzipha pogwiritsa ntchito mankhwala oopsa ophera tizilombo, koma wati akudikira lipoti lachipatala kuti atsimikize chomwe chayambitsa imfayi.

Mwalwanda amachokera m'mudzi mwa Mwahimba, mwa mfumu yayikulu Mwakisamba, m'boma la Karonga.

Yao traditional leaders say preparations for this year’s Chiwanja cha Yao Cultural gathering, scheduled for October 10, ...
02/10/2026

Yao traditional leaders say preparations for this year’s Chiwanja cha Yao Cultural gathering, scheduled for October 10, 2026 in Salima District, are nearing completion.

Senior Chief Chowe, Secretary of the Chiwanja cha Yao Council, says this year’s gathering will focus on addressing rising cases of child marriage in areas where the Yao community is found.

Chowe says the gathering will also discuss ways of improving girls’ access to education, particularly those facing challenges in accessing financial and other support to remain in school.

Meanwhile Child rights activist Memory Ngosi has welcomed the focus, but says the gathering should go beyond discussions and result in concrete action to reduce child marriages and promote girls’ education.

Ngosi says other communities can borrow a leaf from the Yao’s efforts to develop strategies against child marriage, urging leaders to turn discussions into practical measures that protect girls and keep them in school.

Ku Monkey Bay, bambo wa zaka 48, a Cassim Chiwaya, amugamula kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zitatu (8) kaamba k...
02/10/2026

Ku Monkey Bay, bambo wa zaka 48, a Cassim Chiwaya, amugamula kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zitatu (8) kaamba kogwililira mwana wa mkazi wa zaka khumi ndi zitatu (13).

Woyimira boma pa milandu, a Lyson Kachikondo, anauza bwalo lamilandu la Monkey Bay lero kuti bamboyu anapalamula mlanduwu pa 1 September chaka chino, nthawi ya 5 koloko madzulo, m'mudzi wa Mtola.

A Kachikondo ati patsikuli, mwanayu amachokera kowonera kanema (video show), ndipo anakumana ndi bamboyu yemwe anayamba kumulondola.

"Atangoyenda pang'ono, bamboyu anamukokera mwanayu pa tchire pomwe anamugwililira. Mwanayu anakuwa, koma anthu sanamve ndipo palibe anabwera kudzamupulumutsa," iwo atero.

Popereka chigamulo chake, woweruza milandu a Roy Kakutu anati bamboyu sanawonetse chitsanzo chabwino, ndipo akuyenera kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zitatu (8).

Amagwira ntchito yanji awa šŸ¤”
02/10/2026

Amagwira ntchito yanji awa šŸ¤”

A record number of people in Yemen are unable to meet their food needs as conflict intensifies in the country, the World...
02/10/2026

A record number of people in Yemen are unable to meet their food needs as conflict intensifies in the country, the World Food Programme said on Friday.

Within a few weeks, three in four households in government-controlled areas that are accessible to the WFP would be skipping meals, Matthew Hollingworth, the agency’s assistant executive director, told reporters in Geneva via video link from Rome.

The population of government-held areas is estimated at about 10 million.

ā€œThe effect of this latest flare-up of insecurity on the food security situation threatens to be absolutely devastating,ā€ Hollingworth said.

Breaking News šŸ¤•Wamwalira atalephera kutsata ndondomeko yokulitsa Nyash yakešŸ’”TikToker Fatima waku Nigeria ali mkati mopan...
02/10/2026

Breaking News šŸ¤•

Wamwalira atalephera kutsata ndondomeko yokulitsa Nyash yakešŸ’”

TikToker Fatima waku Nigeria ali mkati mopanga BBL Nyash yake inayamba kutuluka mafinya mpaka Doctor analephera kumuchiza pakuti anazindikira mochedwa kuti mankhwala omwe anamuika mu ma hip ake kuti Nyash izikula anasiya kugwira ntchito

May her soul rest in peace

Nepal plans to drain four glacial lakes after deadly floods
02/10/2026

Nepal plans to drain four glacial lakes after deadly floods

Address

Eastern Cape
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Emmanuel Chisawa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share