18/09/2025
BREAKING NEWS: CHAKWERA NDI AKULUAKULU ACHIPANI CHA MCP AKUKAMBILANABE ZA NJIRA ZOMUGONJETSELA MUNTHARIKA KUTI ASATENGE BOMA
Mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera ndi akuluakulu achipani chake cha, Malawi Congress Party MCP akukambilana za njira zomwe angagwilitse ntchito kuti amugonjetse mtsogoleri wachipani cha, Democratic Progressive Party DPP, Professor Arthur Peter Muntharika.
Chigawo chakumasana kuno akuluakuku achipani cha, MCP anagwilizana mfundo yoti achonge ma ballot paper oposela, 3 Million ndipo akamaliza awatenge ndikukasinthanitsa ndima ballot omwe ayikidwe kuma warehouse achigawo chapakati ndikumpoto. Iwo anati akachita izi, Mtalimanja azaweluze kuti zisankho sizinatende bwino ndipo ziwelengedweso. Kachiwiriko akazawelengela asazachedwe kuwulutsa ndikumutengela, Chakwera ku, Bingu National Stadium kuti akalumbilitsidwe.
Mfundo inanso inali yoti amange gulu la, Shadreck Namalomba, Norman Chisale, Sameer Suleiman ndi anzawo ena ndikuwatsegulira milandu yaboza yoti amafuna kuwukila boma la Chakwera komanso abela zisankho.
Pakadali pano zosatila zosasikimizika zikusonyeza kuti,Muntharika ndiye akuwina ndimavote oposela 70%
Manna News Online