29/07/2025
28 July 2025
Chipani cha Assembly for Democracy and Development - *ADD* chikudziwitsa onse kuti mtsogoleri wachipanichi *Rt. Honorable Dr Cassim Chilumpha Sc* wachiwili opuma kwa mtsogoleri wakale wadziko la *Malawi* sapeleka zikalata zake ku bungwe loona za chisankho la *MEC* pa 29 July 2025 monga zinaliri popikisananawo pampando wa pulezidenti
Iwo apanga chisankho chogwila ntchito ndikulowa mu mgwilizano omwe akutsogolera Mai *Dr Joyce Banda* mtsogoleri wakale wadziko la *Malawi* yemwe ndi mtsogoleri wachipani cha People's Party - *PP*
Iwo akupempha ma membala awo onse mdziko muno komaso aMalawi akufuna kwabwino kuti pachisankho chikubwelachi pa 16 September 2025 tidzasankhe Mai *Dr Joyce Banda* kukhala mtsogoleri wadziko lino kudzela mu *Luntha* lomwe alinalo pakayendetsedwe kadziko ndimabungwe omwe asali aboma
*NDIZOTHEKA NDI MAI DR JOYCE BANDA*
Lameck Sapuwa
0993853998
Ofalitsa Nkhani mchipani cha
Assembly for Democracy and Development - *ADD*