Cavi's Library

Cavi's Library Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Cavi's Library, Library, Mchinji.

25/06/2022

Yesterday I met a guy standing behind an electricity pole. Surprisingly he was just looking at his right. Then I decided to ask him why....

"Am just looking at the right because my wife left me" he said

Then I was like "Now look at the left because what she did was right"

Now am on the bed at the hospital but I don't know how come to be found here🤣🤣

22/06/2022

" A Joe tamapangani changu man mufuna kuti chakudya asatiwerengere kapena?"

"Aa easy iwe watani Kodi? Ndisavale? Ndikubwera tangodikira pang'ono.

Iyitu inali nthawi yomwe ifeyo nda Joe timakonzekera ulendo wopita Kwa Tapiwa; chibwezi Cha Joe. A Joe adaitanidwa ndi a bea awo kuti akacheze kunyumba kwao. Nde ife monga a bestie a Joe tinangoyenera kupita nawo basi.

"Ndamalizatu man titha kuuyamba apa"

"Aaa iwe ndiwoswa nyerere Kodi?"

"Eyaka, njingatu atenga masiteni avaya nayo kuchigayo"

"Shaaaa"

"Bwanji? Utsala kapena?"

"Mayazi, kungoti..... Basi tiyeni bola tikadyeko nyama kumeneko coz sindingangoyenda pabule.

Tinauyambatu ulendo wa Kwa Tapiwa. Nde kunali dzuwa la phwe. Titayandikira a Joe anamudziwitsa Tapi kuti tayandikira pa kwao nde atichingamire pa gate.

"Inu ine ndikuphika sindingathe kutero just come bola mufike basi mix kulibe makolo onse Ali kuntchito nde mungolowa"

Apa nde tinadziwa kuti sitikafinyikako uku because kulibe akulu. Titafika nde zinali za bhobho. Anatilandira bwino ndikutilowetsa mu deni yawo.

"Aise Tapi tandigaireko madzi aise ludzu landiswa koposa"

"Madzi kapena drink?"

A Joe anangodzayankha mwachangu kuti abweretse drink yo basi.

Titacheza pang'ono alarm inadzalira ya 12 noon (mudziwa za ana akumpanda).Kenako Tapiwa adadzangoti ndikubwera. Within ma seconds adabwera ndi mpunga amwene kudzadza ma food warmer awiri plus ma soft drink 2 bottles. Ine mtima unachita kudumphira mmwamba amwene mix chimpunga chimanunkhira ichi guys.

"This is the food ma guys ndikubwera pompano"

Ife sibasi mkugawana ma foodwarmer aja one one man.

"A Kavi mumaliza koma chakudya chonsechi?"

"Aa iwe Joe ukutanthauza chani ukatero? Iweyo sumaliza kapena? Undipatse ngati sumaliza coz ineyo nde njala yandikudzula msaname".

"mmm man foodaz yonseyi munthu angamalize mkumafunaso Ina? Utumbidwa chani?"

Tinagaya chakudya mpaka mmimba kunvaso kuti ntchito yagwirika apa. Pena ngati ndisiye kudya koma mmati mkanva kafungo si...

Part 2 loading..

Address

Mchinji

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cavi's Library posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Cavi's Library:

Share

Category