Mangochi District Council

Mangochi District Council Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mangochi District Council, Government Organization, Private Bag 138, Mangochi.

This is the Official page for Mangochi District Council, where updates on developmental projects and initiatives by the council, as well as development partners, are shared

ULOSI WA NYENGO YA DZINJA YA 2026/2027Nthambi yoona za nyengo mdziko muno yati madera ambiri a boma la Mangochi akuyembe...
22/09/2026

ULOSI WA NYENGO YA DZINJA YA 2026/2027

Nthambi yoona za nyengo mdziko muno yati madera ambiri a boma la Mangochi akuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepera apo.

Mvula ya mlingo okhazikika ikuyembekezeka kuyambira sabata yoyamba ya mwezi wa December.

Pali chiopsezo cha ng’amba yosachepera sabata imodzi mu mwezi wa January koma masabata awiri mu February.

Nyengo ya dzinja ikuyembekezeka kukhala yotalika ndi masiku a pakati pa 80 ndi 100.

Mvula yokhazikika ikuyembekezeka kupita kumapeto kuyambira sabata yomaliza ya March.

Pezani mwayi wolipiridwa Maphunziro, kuchokela mu thumba la Constituency Development Fund (CDF). Adziwitseni anzanu: Zik...
15/09/2026

Pezani mwayi wolipiridwa Maphunziro, kuchokela mu thumba la Constituency Development Fund (CDF).

Adziwitseni anzanu: Zikutheka!

# MangochiDistrictCouncil

Phungu wa Nyumba ya Malamulo kumwera cha ku zambwe m'boma la Mangochi, yemwenso ndi nduna ya zofalitsa nkhani, a Shadric...
12/09/2026

Phungu wa Nyumba ya Malamulo kumwera cha ku zambwe m'boma la Mangochi, yemwenso ndi nduna ya zofalitsa nkhani, a Shadric Namalomba lero atsekulira chipinda chogona atsikana pa sukulu ya Chilipa Community Day Secondary.

Chipindachi chidzisunga atsikana oposa 50, ndipo chamangidwa ndi ndalama za mu thumba lotchedwa Governance to Enable Service Delivery (GESD), zokwana K 435 million.

Kutsekulira kwa chipindachi kuthandiza kukweza maphunziro a atsikana ku Chilipa, omwe amayenda mitunda Itali Itali kuti apeze maphunziro.

District Council

a atsikana

VACANCIES ANNOUNCEMENTThe Local Government Service Commission is inviting applications from suitably qualified Malawians...
11/09/2026

VACANCIES ANNOUNCEMENT

The Local Government Service Commission is inviting applications from suitably qualified Malawians to fill the posts as indicated below, existing at Mangochi District Council:

OFFICIAL GROUNDBREAKING CEREMONY OF MANGOCHI-MAKANJIRA ROAD BRIDGES
09/09/2026

OFFICIAL GROUNDBREAKING CEREMONY OF MANGOCHI-MAKANJIRA ROAD BRIDGES

01/09/2026
01/09/2026

Mangochi on forest conservation, through the Embassy of Iceland

Head of Mission for Embassy of Iceland, David Bjarnason, toured forest conservation work in Senior Chiefs Chowe and Nankumba, that are supported by Iceland, through Mangochi District Council.

From empowering locals to create assets that buffer against climatic shocks, for community resilience, the mission is also helping to improve livelihoods, through agro-forestry.

As Bjarnason was leaving Chowe on Tuesday, Group Village Chindamba together with his subordinates chanted— _“when going back to Iceland, remember us!”_ — asking for more support.

District Council
of Iceland
conservation

Bungwe la UNICEF lapereka njinga za moto 8, komanso za kapalasa 12 kwa ogwira ntchito ku Khonsolo ya Mangochi, kuti zith...
01/09/2026

Bungwe la UNICEF lapereka njinga za moto 8, komanso za kapalasa 12 kwa ogwira ntchito ku Khonsolo ya Mangochi, kuti zithandizile magulu oyenda m'midzi kufikila mwachangu madera omwe kukadali nchitidwe wokwatitsa ana a ang'ono, ndikuphunzitsa anthu za kuyipa kwa nchitidwewu.

M'modzi wa akuluakulu ku bungweli a Malla Mabona ati thandizoli lili mu pologalamu yolimbana ndi nkhaza kwa ana, komanso kuteteza ma ufulu awo.

"Tapeleka zoyendelazi pofuna kuwonetsetsa kuti palibe mwana yemwe akubwelera m'buyo pa maphunziro. Ma ukwati a ana ang'ono ang'ono akusokoneza atsikana ndi anyamata kuno ku Mangochi," atelo a Mabona.

Mawu awo, nkulu owona za ntchito ku Khonsolo ya Mangochi a Steve Chima ati mwazina, njingazi zithandiza kuphunzitsa anthu za kuchepetsa nchitidwe wa nkhanza za m'banja.

District Council

Wachiwiri kwa Nduna yowona za chilengedwe a Chipiliro Mpinganjira yapeleka ndalama zokwana K500,000 kwa Duwana Muhammad ...
18/08/2026

Wachiwiri kwa Nduna yowona za chilengedwe a Chipiliro Mpinganjira yapeleka ndalama zokwana K500,000 kwa Duwana Muhammad kaamba ka mbiri yake ya maphunziro yomwe yalimbikitsa achinyamata ndi anthu ena.

Naye mkulu wa bungwe la Malawi Bureau of Standards a Symon Mandala sanachitire mwina koma kupeleka ina K500,000 kwa Duwana kaamba ka nkhani yake yomwe inawakhuza.

Izitu sizinathere p***a, pomwe mlembi mu unduna owona za masewero a Jasmeson Ndalama apeleka ndalama ina yokwana K200,000.

Pakadali pano mkulu wa Banki ya Standard a Philip Madinga alonjeza Duwana kuti amutsegulira akaunti ya maphunziro yomwe izisunga ndalamayi.

Izi zachitika lero, pa msonkhano wokambilana za a chinyamata *National Youth Summit* ku Lilongwe.

(Copied: Malawi).

16/08/2026

🎓 Official Maranatha Academy Page
✨ Home of Excellence& Character
📚 Admissions |Scholarships |Student Life
🌍 Raising Future Leaders• Learning
📍Malawi| Meliora Sequamur

Address

Private Bag 138
Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mangochi District Council posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share