Honourable Norman Chisale - DPP National Youth Director

Honourable Norman Chisale - DPP National Youth Director I am Norman Chisale, National Director of Youth for the DPP. I call upon all youths to unite in support of His Excellency Prof.
(2)

Arthur Peter Mutharika as we approach the 2025 general elections. A peaceful and non-violent campaign starts with us, youths!

Komatu muthuyu Ali ndi khope ya chilungamo!
15/09/2026

Komatu muthuyu Ali ndi khope ya chilungamo!

MCP nkhanza1. Ndinamuona Chilimba pakhomo atayima akukodola ndikukuwa2. Chilima ankafuna kudumpha koma ankakokeledwa mka...
15/09/2026

MCP nkhanza

1. Ndinamuona Chilimba pakhomo atayima akukodola ndikukuwa
2. Chilima ankafuna kudumpha koma ankakokeledwa mkati
3. Tinayitsatira ndege mpaka pamene inkagwa
4. Mundegemo mudatuluka anthu awiri
5. Kenako chigulu cha anthu oyera ovala zachisilikali pafupifupi 10 anatulukira pamalopo nkuyamba kuomba mfuti
6. Anthu anatuluka mundege aja anayamba kuwomba mfuti nkumatithamangitsa
7. Pa 11 June ndinangodzindikira ndili muchithumba chachikulu pamodzi ndimunthu wakufa amene ndinali naye patsiku limene tinkatsatira ndege ija, ankaona ngati nanenso andipha ndizipolopolo
8. Ndege itagwa sinaphwanyike

15/09/2026

I warmly invite everyone to come and witness some of the finest talent in our community battling for the K50 Million prize.
Let us come together, support our young people, promote discipline through sport, and celebrate the spirit of unity and development in Ntcheu Central East.
This is our community. This is our talent. This is our day!

See you at Kuyenda Ground!

15/09/2026

Amalawi simunabetse vote yanu. Zambiri zikukonzedwa ndipo pompano vuto la magetsi ndi Forex ikhala mbiri yakale.
Ajawa analionongatu dzikoli.

15/09/2026

Mu chaka chimodzi chokha, His Excellency Professor Arthur Peter Mutharika akwanisa:
1. kuthesa vuto la njala,
2. akwanisa kuthesa vuto lakusowa Kwa fuel,
3. akwaniritsa Lonjezo la school ya ulele,
4. akwanisa Lonjezo la 5 billion per constituency,
5. akwanisa kukweza chuma Cha dziko lino,
6. akwanisa kusitha kuti katundu asamakwere mtengo daily,
7. Sugar akupezeka pali ponse
8. Anthu asiya kuyenda chewu chewu chifukwa Cha zikwanje

Ndiye muona ngati angakanike kuthetsa vuto la kuzima Kwa magetsi? Osatheka, APM is here to deliver, vuto la magetsi ikhala mbiri ya kale. In APM, we believe 🙏 long live APM 🙏😊

NB: President sangakwaniritse chili chonse mu chaka chimodzi ngati ngero🙏

15/09/2026

"koma ndegeyo mene ife tinayionera...." kuyankhula ndi a Cassim Aubi

14/09/2026

Ati akhululukirana koma Tonse Alliance ya 2030 azaimile ndi awo a 200k votes. Zoopsa kobasi.

13/09/2026

C O M M E N T

I remember that as we approached the 2019 elections, the leader of their party came forward to apologize to those who had lost their loved ones because of them. But today, are we seeing the same things happening again?
Sometimes, we Malawians need to learn to remember and hold people accountable. We must not allow ourselves to be taken for granted. We should live with a sense of shame and responsibility.
MCP — NEVER AGAIN!

Ndine wokondwa kuthandiza ana 33 ochokera ku Senior Chief Champiti ndi Senior Chief Makwangwala powalipirira ndalama za ...
13/09/2026

Ndine wokondwa kuthandiza ana 33 ochokera ku Senior Chief Champiti ndi Senior Chief Makwangwala powalipirira ndalama za sukulu zokwana K6.6 miliyoni.

Mwana aliyense walandira K200,000 pa term ino, komanso ndawapatsa masutikesi, makope a hard cover ndi zolembera kuti athe kuphunzira bwino komanso mosavuta.

Ndikhulupirira kuti thandizoli lithandiza kuchepetsa mavuto omwe makolo ena amakumana nawo, makamaka pa nkhani ya ndalama za boarding school.

Kwa ana onsewa, ndikuwalimbikitsa kuti azilimbikira maphunziro, chifukwa maphunziro ndi chinsinsi cha tsogolo labwino. Ndipo ngati adzachita bwino pa maphunziro awo, ndipitiliza kuwathandiza momwe ndingathere.

Tiyeni tonse tigwirizane pothandiza ana athu kuti akhale ndi tsogolo labwino. 🇲🇼❤️

Address

DPP National Secretariat, P. O Box 1618, Naperi
Blantyre
265999492653

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Honourable Norman Chisale - DPP National Youth Director posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share